Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 13:29 - Buku Lopatulika

29 Koma iye anati, Iai, kuti kapena m'mene mukasonkhanitsa namsongoleyo, mungazulenso tirigu pamodzi naye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 Koma iye anati, Iai, kuti kapena m'mene mukasonkhanitsa namsongoleyo, mungazulenso tirigu pamodzi naye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Koma iye adati, ‘Iyai, mungakazulire kumodzi ndi tirigu pozula namsongoleyo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 “Iye anakana nati, ‘Ayi. Chifukwa pamene mukuzula namsongoleyo mwina inu mungazulire pamodzi ndi tirigu.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 13:29
3 Mawu Ofanana  

koma m'mene anthu analinkugona, mdani wake anadza, nafesa namsongole pakati pa tirigu, nachokapo.


Ndipo iye ananena kwa iwo, Munthu mdani wanga wachichita ichi. Ndipo anyamata anati kwa iye, Kodi mufuna tsopano kuti timuke, tikamsonkhanitse uyo pamodzi?


Kazilekeni zonse ziwiri, zikulire pamodzi kufikira pakututa; ndimo m'nyengo yakututa ndidzauza akututawo, Muyambe kusonkhanitsa namsongole, mummange uyu mitolo kukamtentha, koma musonkhanitse tirigu m'nkhokwe yanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa