Mateyu 13:16 - Buku Lopatulika16 Koma maso anu ali odala, chifukwa apenya; ndi makutu anu chifukwa amva. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Koma maso anu ali odala, chifukwa apenya; ndi makutu anu chifukwa amva. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 “Koma inu ndinu odala, popeza kuti maso anu akupenya, ndipo makutu anu akumva. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Koma maso anu ndi odala chifukwa amapenya ndi makutu anu chifukwa amamva. Onani mutuwo |