Mateyu 12:7 - Buku Lopatulika7 Koma mukadadziwa nchiyani ichi, Ndifuna chifundo, si nsembe ai; simukadaweruza olakwa iwo osachimwa, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Koma mukadadziwa nchiyani ichi, Ndifuna chifundo, si nsembe ai; simukadaweruza olakwa iwo osachimwa, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Mukadadziŵa tanthauzo la mau a Mulungu aja akuti, ‘Ndimafuna chifundo, osati nsembe ai,’ sibwenzi mutaweruza kuti ndi olakwa anthu amene sadalakwe konse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ngati mukanadziwa zomwe mawu awa atanthauza, ‘Ine ndifuna chifundo osati nsembe,’ inu simukanatsutsa osalakwa. Onani mutuwo |