Mateyu 12:47 - Buku Lopatulika47 Ndipo munthu anati kwa Iye, Onani, amai wanu ndi abale anu aima pabwalo, nafuna kulankhula nanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Ndipo munthu anati kwa Iye, Onani, amai wanu ndi abale anu aima pabwalo, nafuna kulankhula nanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 Tsono munthu wina adauza Yesu kuti, “Amai anu ndi abale anu ali panjapa, akufuna kulankhula nanu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 Wina anamuwuza Iye kuti, “Amayi ndi abale anu ayima kunjaku akufuna kuyankhulana nanu.” Onani mutuwo |