Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 12:19 - Buku Lopatulika

19 Sadzalimbana, sadzafuula; ngakhale mmodzi sadzamva mau ake m'makwalala;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Sadzalimbana, sadzafuula; ngakhale mmodzi sadzamva mau ake m'makwalala;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Iye sadzachita makani, kapena kufuula. Palibe munthu wodzamva mau ake m'miseu ya m'mizinda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Sadzalimbana, sadzafuwula, ngakhale mmodzi sadzamva mawu ake mʼmakwalala.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 12:19
8 Mawu Ofanana  

Iye sadzafuula, ngakhale kukuwa, pena kumvetsa mau ake m'khwalala.


Kondwera kwambiri, mwana wamkazi wa Ziyoni; fuula mwana wamkazi wa Yerusalemu; taona, Mfumu yako ikudza kwa iwe; ndiye wolungama, ndi mwini chipulumutso; wofatsa ndi wokwera pabulu, ndi mwana wamphongo wa bulu.


Senzani goli langa, ndipo phunzirani kwa Ine; chifukwa ndili wofatsa ndi wodzichepetsa mtima: ndipo mudzapeza mpumulo wa miyoyo yanu.


bango lophwanyika sadzalithyola, ndi nyali yofuka sadzaizima, kufikira Iye adzatumiza chiweruzo chikagonjetse.


Ndipo pamene Afarisi anamfunsa Iye, kuti, Ufumu wa Mulungu ukudza liti, anawayankha, nati, Ufumu wa Mulungu sukudza ndi maonekedwe;


Koma ine ndekha Paulo, ndidandaulira inu mwa kufatsa ndi ulere wa Khristu, ine amene pamaso panu ndikhala wodzichepetsa pakati pa inu, koma pokhala kwina ine ndilimbika mtima kwa inu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa