Mateyu 11:26 - Buku Lopatulika26 eetu, Atate, chifukwa chotero chinakhala chokondweretsa pamaso panu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 etu, Atate, chifukwa chotero chinakhala chokondweretsa pamaso panu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Chabwino Atate, pakuti mudafuna kutero mwa kukoma mtima kwanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Inde, Atate, ichi chinali chokukomerani Inu. Onani mutuwo |