Mateyu 11:18 - Buku Lopatulika18 Pakuti Yohane anadza wosadya, wosamwa, ndipo iwo amati, Ali ndi chiwanda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Pakuti Yohane anadza wosadya, wosamwa, ndipo iwo amati, Ali ndi chiwanda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Paja Yohane Mbatizi atabwera, ankasala zakudya ndi zakumwa, anthu nkumati, ‘Adagwidwa ndi mzimu woipa.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Pakuti Yohane sanabwerere kudya kapena kumwa koma iwo ankanena kuti, ‘Iye anali ndi chiwanda.’ Onani mutuwo |