Mateyu 10:34 - Buku Lopatulika34 Musalingalire kuti ndidadzera kuponya mtendere padziko lapansi; sindinadzere kuponya mtendere, koma lupanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Musalingalire kuti ndidadzera kuponya mtendere pa dziko lapansi; sindinadzera kuponya mtendere, koma lupanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 “Kodi mukuyesa kuti ndidadzapereka mtendere pansi pano? Sindidadzapereke mtendere ai, koma nkhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 “Musaganize kuti Ine ndabweretsa mtendere pa dziko lapansi. Sindinabwere kudzapereka mtendere koma lupanga. Onani mutuwo |