Mateyu 10:24 - Buku Lopatulika24 Wophunzira saposa mphunzitsi wake, kapena kapolo saposa mbuye wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Wophunzira saposa mphunzitsi wake, kapena kapolo saposa mbuye wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Paja wophunzira saposa mphunzitsi wake, ndipo wantchito saposa mbuye wake ai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 “Wophunzira saposa mphunzitsi wake ndipo wantchito saposa bwana wake. Onani mutuwo |