Mateyu 10:20 - Buku Lopatulika20 pakuti wolankhula si ndinu, koma Mzimu wa Atate wanu akulankhula mwa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 pakuti wolankhula si ndinu, koma Mzimu wa Atate wanu akulankhula mwa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Pajatu odzalankhula si ndinu ai, koma Mzimu wa Atate anu ndiye amene adzalankhula kudzera mwa inu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 pakuti sindinu mudzanena, koma Mzimu Woyera wa Atate anu, adzayankhula mwa inu. Onani mutuwo |