Mateyu 10:18 - Buku Lopatulika18 ndiponso adzamuka nanu kwa akazembe ndi mafumu chifukwa cha Ine, kukhala mboni ya kwa iwo, ndi kwa anthu akunja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 ndiponso adzamuka nanu kwa akazembe ndi mafumu chifukwa cha Ine, kukhala mboni ya kwa iwo, ndi kwa anthu akunja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Adzapita nanu kwa nduna ndi mafumu chifukwa cha Ine, mwakuti mudzandichitira umboni pamaso pao, ndi pa anthu a mitundu ina. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Chifukwa cha Ine, mudzaperekedwa kwa olamulira ndi kwa mafumu kuti mukhale mboni kwa iwo ndi kwa a mitundu ina. Onani mutuwo |