Mateyu 1:25 - Buku Lopatulika25 ndipo sanamdziwe iye kufikira atabala mwana wake; namutcha dzina lake Yesu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 ndipo sanamdziwe iye kufikira atabala mwana wake; namutcha dzina lake Yesu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 koma sadamdziŵe mpaka adabala mwana wamwamuna. Pambuyo pake Yosefe adatcha mwanayo dzina loti Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Koma sanagone malo amodzi mpaka mwanayo atabadwa ndipo anamutcha dzina lake Yesu. Onani mutuwo |