Mateyu 1:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo Yosefe anauka tulo take, nachita monga anamuuza mngelo wa Ambuye, nadzitengera yekha mkazi wake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo Yosefe anauka tulo take, nachita monga anamuuza mngelo wa Ambuye, nadzitengera yekha mkazi wake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Tsono Yosefe atadzuka, adachita monga momwe mngelo wa Ambuye uja adaamuuzira. Adamtenga Maria, mkazi wake uja, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Yosefe atadzuka, anachita zomwe mngelo wa Ambuye uja anamulamulira. Iye anamutenga Mariya kukhala mkazi wake. Onani mutuwo |