Masalimo 96:9 - Buku Lopatulika9 Gwadirani Yehova moyera ndi mokometsetsa, njenjemerani pamaso pake, inu dziko lonse lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Gwadirani Yehova moyera ndi mokometsetsa, njenjemerani pamaso pake, inu dziko lonse lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pembedzani Chauta waulemerero ndi woyera, njenjemerani pamaso pake, inu anthu onse a pa dziko lapansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Lambirani Yehova mu ulemerero wa chiyero chake; njenjemerani pamaso pake, dziko lonse lapansi. Onani mutuwo |