Masalimo 96:11 - Buku Lopatulika11 Kumwamba kukondwere nilisekerere dziko lapansi; nyanja ibume mwa kudzala kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Kumwamba kukondwere nilisekerere dziko lapansi; nyanja ibume mwa kudzala kwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Zakumwamba zisangalale, zapansi pano zikondwere, nyanja ikokome pamodzi ndi zonse zam'menemo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Mayiko akumwamba asangalale, dziko lapansi likondwere; nyanja ikokome, ndi zonse zili mʼmenemo; Onani mutuwo |