Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 90:9 - Buku Lopatulika

9 Pakuti masiku athu onse apitirira mu ukali wanu; titsiriza moyo wathu ngati lingaliro.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Pakuti masiku athu onse apitirira m'ukali wanu; titsiriza moyo wathu ngati lingaliro.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Pajatu masiku athu amachepa chifukwa cha mkwiyo wanu, zaka zathu zimatha ngati kuusa moyo chabe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Masiku athu onse amatha ali pansi pa ukali wanu; timatsiriza zaka zathu ndi kubuwula.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 90:9
5 Mawu Ofanana  

Akhale monga mungu kumphepo, ndipo mngelo wa Yehova awapirikitse.


Imvani pemphero langa, Yehova, ndipo tcherani khutu kulira kwanga; musakhale chete pa misozi yanga; Pakuti ine ndine mlendo ndi Inu, wosakhazikika, monga makolo anga onse.


Onani, munaika masiku anga akhale monga kuyesa dzanja; ndipo zaka zanga zili ngati chabe pamaso panu, Indedi munthu aliyense angakhale wokhazikika, ali chabe konse.


Potero anathera masiku ao ndi zopanda pake, ndi zaka zao mwa mantha.


Pakuti pamaso panu zaka zikwi zikhala ngati dzulo, litapita, ndi monga ulonda wa usiku.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa