Masalimo 90:4 - Buku Lopatulika4 Pakuti pamaso panu zaka zikwi zikhala ngati dzulo, litapita, ndi monga ulonda wa usiku. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pakuti pamaso panu zaka zikwi zikhala ngati dzulo, litapita, ndi monga ulonda wa usiku. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Pakuti zaka chikwi chimodzi pamaso panu zili ngati dzulo chabe, kapena ngati kamphindi chabe kausiku. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Pakuti zaka 1,000 pamaso panu zili ngati tsiku limene lapita kapena ngati kamphindi ka usiku. Onani mutuwo |