Masalimo 78:51 - Buku Lopatulika51 Ndipo anapha ana oyamba onse a mu Ejipito, ndiwo oyamba a mphamvu yao m'mahema a Hamu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201451 Ndipo anapha ana oyamba onse a mu Ejipito, ndiwo oyamba a mphamvu yao m'mahema a Hamu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa51 Adapha ana achisamba onse a Aejipito, ana oyamba a mphamvu zao, m'zithando za zidzukulu za Hamu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero51 Anakantha ana oyamba kubadwa a Igupto, zipatso zoyamba kucha za mphamvu zawo mʼmatenti a Hamu Onani mutuwo |