Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 78:16 - Buku Lopatulika

16 Anatulukitsa mitsinje m'thanthwe, inde anatsikitsa madzi ngati mitsinje.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Anatulukitsa mitsinje m'thanthwe, inde anatsikitsa madzi ngati mitsinje.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Adatumphutsa mifuleni m'thanthwe, nayendetsa madzi ngati mitsinje.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Anatulutsa mitsinje kuchokera mʼmingʼalu ya miyala ndi kuyenda madzi ngati mitsinje.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:16
9 Mawu Ofanana  

Anatsegula pathanthwe, anatulukamo madzi; nayenda pouma ngati mtsinje.


Asanduliza chipululu chikhale thawale, ndi dziko louma likhale akasupe a madzi.


Unjenjemere, dziko lapansi iwe, pamaso pa Ambuye, pamaso pa Mulungu wa Yakobo;


amene anasanduliza thanthwe likhale thawale lamadzi, nsangalabwi ikhale kasupe wamadzi.


Munapombosola uta wanu; malumbiro analumbirira mafuko anali mau oona. Munang'amba dziko lapansi ndi mitsinje.


Tenga ndodoyo, nusonkhanitse khamulo; iwe ndi Aroni mbale wako, munene ndi thanthwe pamaso pao, kuti liwapatse madzi; potero uwatulutsire madzi m'thanthwe, ndi kumwetsa khamu la anthu ndi zoweta zao.


amene anakutsogolerani m'chipululu chachikulu ndi choopsacho, munali njoka zamoto, ndi zinkhanira, mouma mopanda madzi; amene anakutulutsirani madzi m'thanthwe lansangalabwi;


Ndipo ndinatenga tchimo lanu, mwanawang'ombe mudampangayo, ndi mumtentha ndi moto, ndi kumphwanya, ndi kumpera bwino kufikira atasalala ngati fumbi; ndipo ndinataya fumbi lake m'mtsinje wotsika m'phirimo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa