Masalimo 72:9 - Buku Lopatulika9 Okhala m'chipululu adzagwadira pamaso pake; ndi adani ake adzaluma nthaka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Okhala m'chipululu adzagwadira pamaso pake; ndi adani ake adzaluma nthaka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Amaliwongo akuchipululu adzaiŵeramira, adani ake adzadya fumbi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mafuko a mʼchipululu adzawerama pamaso pake ndipo adani ake adzanyambita fumbi. Onani mutuwo |