Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 71:8 - Buku Lopatulika

8 M'kamwa mwanga mudzadzala lemekezo lanu, ndi ulemu wanu tsiku lonse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 M'kamwa mwanga mudzadzala lemekezo lanu, ndi ulemu wanu tsiku lonse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Pakamwa panga pakutamanda Inu, pakulalika ulemerero wanu tsiku lonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Pakamwa panga padzaza ndi matamando anu, kulengeza ulemerero wanu tsiku lonse.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 71:8
9 Mawu Ofanana  

Lemekeza Yehova, moyo wanga; Yehova, Mulungu wanga, Inu ndinu wamkulukulu;


Ndidzalemekeza Yehova m'moyo mwanga; ndidzaimbira zomlemekeza Mulungu wanga pokhala ndi moyo ine.


Ndipo lilime langa lilalikire chilungamo chanu, ndi lemekezo lanu tsiku lonse.


Mudzakhutitsa moyo wanga ngati ndi mafuta ndi zonona; ndipo pakamwa panga ndidzakulemekezani ndi milomo yakufuula mokondwera.


Pakamwa panga padzafotokozera chilungamo chanu, ndi chipulumutso chanu tsiku lonse; pakuti sindidziwa mawerengedwe ake.


Lilime langa lomwe lidzalankhula za chilungamo chanu tsiku lonse, pakuti ofuna kundichitira choipa achita manyazi, nadodoma.


Pamaso pake pali ulemu ndi ukulu. M'malo opatulika mwake muli mphamvu ndi zochititsa kaso.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa