Masalimo 71:7 - Buku Lopatulika7 Ndikhala chodabwitsa kwa ambiri; koma Inu ndinu pothawira panga polimba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndikhala chodabwitsa kwa ambiri; koma Inu ndinu pothawira panga polimba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ndakhala chinthu chodabwitsa kwa anthu ambiri, koma Inu ndinu wonditchinjiriza wamphamvu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ine ndakhala chinthu chodabwitsa kwa anthu ambiri koma Inu ndinu wonditchinjiriza wamphamvu. Onani mutuwo |