Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 7:11 - Buku Lopatulika

11 Mulungu ndiye Woweruza wolungama, ndiye Mulungu wakukwiya masiku onse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Mulungu ndiye Woweruza wolungama, ndiye Mulungu wakukwiya masiku onse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Mulungu ndiye muweruzi wolungama, amalanga anthu oipa nthaŵi zonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Mulungu amaweruza molungama, Mulungu amene amaonetsa ukali wake tsiku ndi tsiku.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 7:11
6 Mawu Ofanana  

Ndipo zakumwamba zionetsera chilungamo chake; pakuti Mulungu mwini wake ndiye woweruza.


Yehova aweruza anthu mlandu; mundiweruze, Yehova, monga mwa chilungamo changa, ndi ungwiro wanga uli mwa ine.


Pakuti chiweruzo chidzabwera kunka kuchilungamo, ndipo oongoka mtima onse adzachitsata.


Yehova ndiye Mulungu wansanje, nabwezera chilango; Yehova ndiye wobwezera chilango, ndi waukali ndithu; Yehova ndiye wobwezera chilango oyambana naye, nasungira mkwiyo pa adani ake.


Adzaima ndani pa kulunda kwake? Ndipo adzakhalitsa ndani pa mkwiyo wake wotentha? Ukali wake utsanulidwa ngati moto, ndi matanthwe asweka ndi Iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa