Masalimo 69:7 - Buku Lopatulika7 Pakuti ndalola chotonza chifukwa cha Inu, chimpepulo chakuta nkhope yanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Pakuti ndalola chotonza chifukwa cha Inu, chimpepulo chakuta nkhope yanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Pakuti ndanyozedwa, nkhope yanga yagwidwa ndi manyazi chifukwa cha Inu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Pakuti ndimapirira kunyozedwa chifukwa cha Inu, ndipo manyazi amaphimba nkhope yanga. Onani mutuwo |