Masalimo 69:5 - Buku Lopatulika5 Mulungu, mudziwa kupusa kwanga; ndipo kutsutsika kwanga sikubisikira Inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Mulungu, mudziwa kupusa kwanga; ndipo kutsutsika kwanga sikubisikira Inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Inu Mulungu, mumadziŵa kupusa kwanga, zolakwa zanga sizili zobisika pamaso panu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mukudziwa uchitsiru wanga, Inu Mulungu, kulakwa kwanga sikuli kobisika kwa Inu. Onani mutuwo |