Masalimo 66:13 - Buku Lopatulika13 Ndidzalowa m'nyumba yanu ndi nsembe zopsereza, ndidzakuchitirani zowinda zanga, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndidzalowa m'nyumba yanu ndi nsembe zopsereza, ndidzakuchitirani zowinda zanga, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Ndidzabwera ku Nyumba yanu ndi nsembe zopsereza, ndidzachitadi zimene ndidazilumbira kwa Inu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ine ndidzabwera ku Nyumba yanu ndi nsembe zopsereza ndi kukwaniritsa malumbiro anga. Onani mutuwo |