Masalimo 61:1 - Buku Lopatulika1 Imvani mfuu wanga, Mulungu; mverani pemphero langa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Imvani mfuu wanga, Mulungu; mverani pemphero langa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Inu Mulungu, imvani kulira kwanga, mverani pemphero langa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Imvani kulira kwanga, Inu Mulungu; mvetserani pemphero langa. Onani mutuwo |