Masalimo 52:5 - Buku Lopatulika5 Potero Mulungu adzakupasula kunthawi zonse, adzakuchotsa nadzakukwatula m'hema mwako, nadzakuzula, kukuchotsa m'dziko la amoyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Potero Mulungu adzakupasula kunthawi zonse, adzakuchotsa nadzakukwatula m'hema mwako, nadzakuzula, kukuchotsa m'dziko la amoyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Koma Mulungu adzakutswanya kosalekeza, adzakugwira ndi kukutulutsira kunja kwa nyumba yako. Adzakuzula m'dziko la anthu amoyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Zoonadi Mulungu adzakutsitsa kupita ku chiwonongeko chamuyaya: iye adzakukwatula ndi kukuchotsa mʼtenti yako; iye adzakuzula kuchoka mʼdziko la amoyo. Onani mutuwo |