Masalimo 52:3 - Buku Lopatulika3 Ukonda choipa koposa chokoma; ndi bodza koposa kunena chilungamo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ukonda choipa koposa chokoma; ndi bodza koposa kunena chilungamo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Umakonda zoipa kupambana zabwino, umakonda kunama kupambana kulankhula zoona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Iwe umakonda choyipa mʼmalo mwa kuyankhula choonadi. Umakonda kunama kupambana kuyankhula zoona. Sela Onani mutuwo |