Masalimo 52:1 - Buku Lopatulika1 Udzitamandiranji ndi choipa, chiphona iwe? Chifundo cha Mulungu chikhala tsiku lonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Udzitamandiranji ndi choipa, chiphona iwe? Chifundo cha Mulungu chikhala tsiku lonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Bwanji ukunyadira ntchito zako zoipa, munthu wamphamvuwe? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Nʼchifukwa chiyani ukudzitamandira ndi zoyipa, iwe munthu wamphamvu? Nʼchifukwa chiyani ukudzitamandira tsiku lonse, iwe munthu wochititsa manyazi pamaso pa Mulungu? Onani mutuwo |