Masalimo 51:18 - Buku Lopatulika18 Chitirani Ziyoni chokoma monga mwa kukondwera kwanu; mumange malinga a miyala a Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Chitirani Ziyoni chokoma monga mwa kukondwera kwanu; mumange malinga a miyala a Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Muŵachitire zabwino anthu a ku Ziyoni, chifukwa cha kukoma mtima kwanu. Mumangenso kachiŵiri makoma a Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Mwa kukoma mtima kwanu mupange Ziyoni kuti alemere; mumange makoma a Yerusalemu. Onani mutuwo |