Masalimo 44:1 - Buku Lopatulika1 Mulungu, tidamva m'makutu mwathu, makolo athu anatisimbira, za ntchitoyo mudaichita masiku ao, masiku akale. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Mulungu, tidamva m'makutu mwathu, makolo athu anatisimbira, za ntchitoyo mudaichita masiku ao, masiku akale. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Inu Mulungu, ife tidamva ndi makutu athu, makolo athu adatiwuza za ntchito zimene mudagwira pa masiku ao, masiku amakedzana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ife tamva ndi makutu athu, Inu Mulungu; makolo athu atiwuza zimene munachita mʼmasiku awo, masiku akalekalewo. Onani mutuwo |