Masalimo 39:6 - Buku Lopatulika6 Indedi munthu ayenda ngati mthunzi; Indedi avutika chabe: Asonkhanitsa chuma, ndipo sadziwa adzachilandira ndani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Indedi munthu ayenda ngati mthunzi; Indedi avutika chabe: Asonkhanitsa chuma, ndipo sadziwa adzachilandira ndani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Zoonadi, munthu amayenda ngati chithunzithunzi, amangovutika ndi zachabechabe. Munthu amakundika chuma, koma amene adzachidye ndi wosadziŵika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Munthu ali ngati chithunzithunzi chake pamene akuyenda uku ndi uku: Iye amangovutika koma popanda phindu; amadzikundikira chuma, osadziwa kuti chidzakhala chayani. Onani mutuwo |