Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 34:6 - Buku Lopatulika

6 Munthu uyu wozunzika anafuula, ndipo Yehova anamumva, nampulumutsa m'masautso ake onse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Munthu uyu wozunzika anafuula, ndipo Yehova anamumva, nampulumutsa m'masautso ake onse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Munthu wosaukayu adalira, ndipo Chauta adamumva, nampulumutsa m'mavuto ake onse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Munthu wosauka uno anayitana, ndipo Yehova anamumva; Yehova anamupulumutsa ku mavuto ake onse.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 34:6
10 Mawu Ofanana  

mthenga amene anandiombola ine ku zoipa zonse, adalitse anyamatawa; dzina langa litchulidwe pa iwo, ndi dzina la makolo anga Abrahamu ndi Isaki; iwo akule, nakhale khamu pakati padziko lapansi.


Ndipo Davide analankhula kwa Yehova mau a nyimbo iyi tsikuli Yehova anampulumutsa m'dzanja la adani ake onse, ndi m'dzanja la Saulo.


Yehova, mwamva chikhumbo cha ozunzika, mudzakhazikitsa mtima wao, mudzatchereza khutu lanu;


Ndifuula kwa Yehova ndi mau anga, ndipo andiyankha m'phiri lake loyera.


Ndipo ine ndine wozunzika ndi waumphawi; koma Ambuye andikumbukira ine. Inu ndinu mthandizi wanga, ndi Mpulumutsi wanga, musamachedwa, Mulungu wanga.


munamva mau anga; musabise khutu lanu popuma ndi pofuula ine.


Ndipo iye anati, Mumkomere mtima mdzakazi wanu. Chomwecho mkaziyo anamuka, nakadya, ndi nkhope yake siinakhalanso yachisoni.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa