Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 31:4 - Buku Lopatulika

4 Mundionjole mu ukonde umene ananditchera mobisika. Pakuti Inu ndinu mphamvu yanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Mundionjole m'ukonde umene ananditchera mobisika. Pakuti Inu ndinu mphamvu yanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Onjoleni mu ukonde umene anditchera, pakuti Inu ndinu pothaŵira panga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Ndimasuleni mu msampha umene anditchera pakuti ndinu pothawirapo panga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 31:4
11 Mawu Ofanana  

Moyo wathu unaonjoka ngati mbalame mu msampha wa msodzi; msampha unathyoka ndi ife tinaonjoka.


Odzikuza ananditchera msampha, nandibisira zingwe; anatcha ukonde m'mphepete mwa njira; ananditchera makwekwe.


Ndidzaitanira Yehova, woyenera kutamandika, ndipo adzandipulumutsa ine kwa adani anga.


Mau a m'kamwa mwanga ndi maganizo a m'mtima wanga avomerezeke pamaso panu, Yehova, thanthwe langa, ndi Mombolo wanga.


Atsitsimutsa moyo wanga; anditsogolera m'mabande a chilungamo, chifukwa cha dzina lake.


Maso anga alinga kwa Yehova kosaleka; pakuti Iye adzaonjola mapazi anga mu ukonde.


Pakuti ananditchera ukonde wao m'mbunamo kopanda chifukwa, anakumbira moyo wanga dzenje kopanda chifukwa.


Ananditchera ukonde apo ndiyenda; moyo wanga wawerama. Anandikumbira mbuna patsogolo panga; anagwa m'kati mwake iwo okha.


Wosyasyalika mnzake atcherera mapazi ake ukonde.


Ndipo ananena kwa ine, Chisomo changa chikukwanira; pakuti mphamvu yanga ithedwa mu ufooko. Chifukwa chake makamaka ndidzadzitamandira mokondweratu m'mafooko anga, kuti mphamvu ya Khristu ikhale pa ine.


ndipo akadzipulumutse kumsampha wa mdierekezi, m'mene anagwidwa naye, kuchifuniro chake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa