Masalimo 30:12 - Buku Lopatulika12 kuti ulemu wanga uimbire Inu, wosakhala chete. Yehova Mulungu wanga, ndidzakuyamikani nthawi zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 kuti ulemu wanga uimbire Inu, wosakhala chete. Yehova Mulungu wanga, ndidzakuyamikani nthawi zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Choncho ndisakhale chete, koma ndikutamandeni ndi mtima wonse. Choncho mtima wanga udzakuimbirani mosalekeza, Chauta, Mulungu wanga, ndidzakuthokozani mpaka muyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 kuti mtima wanga uthe kuyimbira Inu usakhale chete. Yehova Mulungu wanga, ndidzapereka kwa Inu mayamiko kwamuyaya. Onani mutuwo |