Masalimo 31:1 - Buku Lopatulika1 Ndakhulupirira Inu, Yehova, ndikhale wopanda manyazi nthawi zonse, mwa chilungamo chanu ndipulumutseni ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndakhulupirira Inu, Yehova, ndikhale wopanda manyazi nthawi zonse, mwa chilungamo chanu ndipulumutseni ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Ndimathaŵira kwa Inu Chauta, musalole kuti ndichite manyazi, koma mundipulumutse chifukwa ndinu Mulungu wolungama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mwa Inu Yehova, ine ndimathawiramo; musalole nʼkomwe kuti ndichititsidwe manyazi; mundipulumutse chifukwa cha chilungamo chanu. Onani mutuwo |