Masalimo 27:7 - Buku Lopatulika7 Imvani, Yehova, liu langa pofuula ine; mundichitirenso chifundo ndipo mundivomereze. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Imvani, Yehova, liu langa pofuula ine; mundichitirenso chifundo ndipo mundivomereze. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Imvani, Inu Chauta, pamene ndikulira mofuula, mundikomere mtima ndi kundiyankha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Imvani mawu anga pamene ndiyitana Inu Yehova mundichitire chifundo ndipo mundiyankhe. Onani mutuwo |