Masalimo 144:3 - Buku Lopatulika3 Yehova, munthu ndani kuti mumdziwa? Mwana wa munthu kuti mumsamalira? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Yehova, munthu ndani kuti mumdziwa? Mwana wa munthu kuti mumsamalira? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Inu Chauta, kodi munthu nchiyani, kuti muzimsamala? Mwana wa munthu nchiyani, kuti muzimganizira? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Inu Yehova, munthu nʼchiyani kuti mumamusamalira, mwana wa munthu kuti muzimuganizira? Onani mutuwo |