Masalimo 142:4 - Buku Lopatulika4 Penyani kudzanja lamanja ndipo muone; palibe wondidziwa; pothawirapo pandisowa; palibe mmodzi wosamalira moyo wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Penyani kudzanja lamanja ndipo muone; palibe wondidziwa; pothawirapo pandisowa; palibe mmodzi wosamalira moyo wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ndikayang'ana ku dzanja lamanja, palibe ndi mmodzi yemwe wosamalako za ine. Kulibe koti ndithaŵire, palibe munthu wondisamala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Yangʼanani kumanja kwanga ndipo onani; palibe amene akukhudzika nane. Ndilibe pothawira; palibe amene amasamala za moyo wanga. Onani mutuwo |