Masalimo 136:5 - Buku Lopatulika5 Amene analenga zakumwamba mwanzeru; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Amene analenga zakumwamba mwanzeru; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Adalenga zakumwamba ndi nzeru zake, pakuti chikondi chake nchamuyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Amene mwachidziwitso chake anapanga mayiko akumwamba, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya. Onani mutuwo |