Masalimo 136:2 - Buku Lopatulika2 Yamikani Mulungu wa milungu; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Yamikani Mulungu wa milungu; pakuti chifundo chake nchosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Thokozani Mulungu wa milungu, pakuti chikondi chake nchamuyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Yamikani Mulungu wa milungu. Pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya. Onani mutuwo |