Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 119:3 - Buku Lopatulika

3 inde, sachita chosalungama; ayenda m'njira zake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 inde, sachita chosalungama; ayenda m'njira zake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 amene sachita zolakwa, koma amayenda m'njira za Chauta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Sachita cholakwa chilichonse; amayenda mʼnjira zake.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:3
5 Mawu Ofanana  

Akamvera ndi kumtumikira, adzatsiriza masiku ao modala, ndi zaka zao mokondwera.


koma chinthu ichi ndinawauza, kuti, Mverani mau anga, ndipo ndidzakhala Mulungu wanu, ndipo inu mudzakhala anthu anga; nimuyende m'njira yonse imene ndakuuzani inu, kuti chikukomereni.


naletsa dzanja lake pa wozunzika, wosalandira phindu kapena choonjezerapo, wochita maweruzo anga, nayenda m'malemba anga; uyu sadzafera mphulupulu ya atate wake, adzakhala ndi moyo ndithu.


Yense wobadwa kuchokera mwa Mulungu sachita tchimo, chifukwa mbeu yake ikhala mwa iye; ndipo sangathe kuchimwa, popeza wabadwa kuchokera mwa Mulungu.


Tidziwa kuti yense wobadwa kuchokera mwa Mulungu sachimwa, koma iye wobadwa kuchokera mwa Mulungu adzisunga yekha, ndipo woipayo samkhudza.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa