Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 119:170 - Buku Lopatulika

170 Kupemba kwanga kudze pamaso panu; mundilanditse monga mwa mau anu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

170 Kupemba kwanga kudze pamaso panu; mundilanditse monga mwa mau anu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

170 Kupempha kwanga kumveke kwa Inu. Mundipulumutse potsata malonjezo anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

170 Kupempha kwanga kufike pamaso panu; pulumutseni molingana ndi lonjezo lanu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:170
9 Mawu Ofanana  

Ndipo tsopano, Yehova Mulungu, mau amene munalankhula za mnyamata wanu ndi za nyumba yake, muwalimbikitse ku nthawi zonse nimuchite monga munalankhula.


Ndipo chifundo chanu chindidzere, Yehova, ndi chipulumutso chanu, monga mwa mau anu.


Ine ndine wanu, ndipulumutseni pakuti ndinafuna malangizo anu.


Mverani mau a kupemba kwanga, pamene ndilirira Inu, pamene ndikweza manja anga kuloza ponenera panu poyera.


Munditcherere khutu lanu; ndipulumutseni msanga. Mundikhalire ine thanthwe lolimba, nyumba yamalinga yakundisunga.


Tsopano tamvanitu, mbuyanga mfumu; pembedzero langa ligwe pamaso panu; kuti musandibwezere kunyumba ya Yonatani mlembi, ndingafe kumeneko.


nati kwa Yeremiya mneneri, Chipembedzero chathu chigwe pamaso panu, nimutipempherere ife kwa Yehova Mulungu wanu, chifukwa cha otsala onsewa; pakuti tatsala ife owerengeka m'malo mwa ambiri, monga maso anu ationa ife;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa