Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:171 - Buku Lopatulika

171 Milomo yanga itulutse chilemekezo; popeza mundiphunzitsa malemba anu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

171 Milomo yanga itulutse chilemekezo; popeza mundiphunzitsa malemba anu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

171 Pakamwa panga padzakutamandani, chifukwa mumandiphunzitsa malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

171 Matamando asefukire pa milomo yanga, pakuti Inu mumandiphunzitsa malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:171
6 Mawu Ofanana  

Ndidzakuyamikani ndi mtima woongoka, pakuphunzira maweruzo anu olungama.


Wopereka nsembe yachiyamiko andilemekeza Ine; ndipo kwa iye wosunga mayendedwe ake ndidzamuonetsa chipulumutso cha Mulungu.


Ambuye, tsegulani pa milomo yanga; ndipo pakamwa panga padzalalikira ulemekezo wanu.


Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira ubwana wanga; ndipo kufikira lero ndilalikira zodabwitsa zanu.


Wodala munthu amene mumlanga, Yehova; ndi kumphunzitsa m'chilamulo chanu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa