Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 119:164 - Buku Lopatulika

164 Ndikulemekezani kasanu ndi kawiri, tsiku limodzi, chifukwa cha maweruzo anu olungama.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

164 Ndikulemekezani kasanu ndi kawiri, tsiku limodzi, chifukwa cha maweruzo anu alungama.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

164 Ndimakutamandani kasanunkaŵiri pa tsiku, chifukwa cha malangizo anu olungama.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

164 Ndimakutamandani kasanu ndi kawiri pa tsiku pakuti malamulo anu ndi olungama.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:164
6 Mawu Ofanana  

Pakati pa usiku ndidzauka kukuyamikani chifukwa cha maweruzo anu olungama.


Likondwere phiri la Ziyoni, asekere ana aakazi a Yuda, chifukwa cha maweruzo anu.


Madzulo, m'mawa, ndi msana ndidzadandaula, ndi kubuula, ndipo adzamva mau anga.


Ziyoni anamva nakondwera, nasekerera ana aakazi a Yuda; chifukwa cha maweruzo anu, Yehova.


Pamenepo anasonkhana anthu awa, napeza Daniele alikupemphera ndi kupembedza pamaso pa Mulungu wake.


pakuti maweruzo ake ali oona ndi olungama; ndipo anaweruza mkazi wachigololo wamkulu, amene anaipsa dziko ndi chigololo chake, ndipo anabwezera chilango mwazi wa akapolo ake padzanja lake la mkaziyo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa