Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 119:163 - Buku Lopatulika

163 Ndidana nalo bodza ndi kunyansidwa nalo; koma ndikonda chilamulo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

163 Ndidana nalo bodza ndi kunyansidwa nalo; koma ndikonda chilamulo chanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

163 Ndimadana ndi anthu abodza, zoonadi, ndimanyansidwa nawo, koma ndimakonda malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

163 Ndimadana ndi chinyengo, kwambiri ndimanyansidwa nacho, koma ndimakonda malamulo anu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:163
13 Mawu Ofanana  

Wakuchita chinyengo sadzakhala m'kati mwa nyumba yanga; wakunena mabodza sadzakhazikika pamaso panga.


Malangizo anu andizindikiritsa; chifukwa chake ndidana nao mayendedwe onse achinyengo.


Ndidana nao a mitima iwiri; koma ndikonda chilamulo chanu.


Chifukwa chake ndiyesa ngolunjika malangizo anu onse akunena zonse; koma ndidana nazo njira zonse zonyenga.


Mundichotsere njira ya chinyengo; nimundipatse mwachifundo chilamulo chanu.


Ndipo ndidzadzikondweretsa nao malamulo anu, amene ndiwakonda.


Wolungama ada mau onama; koma woipa anyansa, nadzichititsa manyazi.


Mundichotsere kutali zachabe ndi mabodza; musandipatse umphawi, ngakhale chuma, mundidyetse zakudya zondiyenera;


Danani nacho choipa, nimukonde chokoma; nimukhazikitse chiweruzo kuchipata; kapena Yehova Mulungu wa makamu adzachitira chifundo otsala a Yosefe.


Chikondano chikhale chopanda chinyengo. Dana nacho choipa; gwirizana nacho chabwino.


Mwa ichi, mutataya zonama, lankhulani zoona yense ndi mnzake; pakuti tili ziwalo wina ndi mnzake.


Kunja kuli agalu ndi anyanga, ndi achigololo, ndi ambanda, ndi opembedza mafano, ndi yense wakukonda bodza ndi kulichita.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa