Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 119:102 - Buku Lopatulika

102 Sindinapatukane nao maweruzo anu; pakuti Inu munandiphunzitsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

102 Sindinapatukana nao maweruzo anu; pakuti Inu munandiphunzitsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

102 Sindisiyana nawo malangizo anu, pakuti Inu mudandiphunzitsa

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

102 Sindinapatuke kuchoka pa malamulo anu, pakuti Inu mwini munandiphunzitsa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 119:102
8 Mawu Ofanana  

Taonani, Mulungu achita mokwezeka mu mphamvu yake, mphunzitsi wakunga Iye ndani?


Pakuti ndasunga njira za Yehova, ndipo sindinachitire choipa kusiyana ndi Mulungu wanga.


Ndipo tsopano ana, mundimvere, musapatuke ku mau a m'kamwa mwanga.


ndipo ndidzapangana nao pangano lamuyaya, kuti sindidzawachokera kuleka kuwachitira zabwino; koma ndidzalonga kuopsa kwanga m'mitima yao, kuti asandichokere.


Ndipo mwa ichinso ife tiyamika Mulungu kosalekeza, kuti, pakulandira mau a Uthenga wa Mulungu, simunawalandire monga mau a anthu, komatu monga momwe ali ndithu, mau a Mulungu, amenenso achita mwa inu okhulupirira.


Anatuluka mwa ife, komatu sanali a ife; pakuti akadakhala a ife akadakhalabe ndi ife, koma kudatero kuti aonekere kuti sali onse a ife.


Ndipo inu, kudzoza kumene munalandira kuchokera kwa Iye, kukhala mwa inu, ndipo simusowa kuti wina akuphunzitseni; koma monga kudzoza kwake kukuphunzitsani za zinthu zonse, ndipo kuli koona, sikuli bodza ai, ndipo monga kudaphunzitsa inu, mukhale mwa Iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa