Masalimo 119:101 - Buku Lopatulika101 Ndinaletsa mapazi anga njira iliyonse yaoipa, kuti ndisamalire mau anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 2014101 Ndinaletsa mapazi anga njira iliyonse yaoipa, kuti ndisamalire mau anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa101 Ndimaletsa miyendo yanga kuti isayende m'njira yoipa iliyonse, kuti choncho ndizisunga mau anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero101 Ndimaletsa miyendo yanga kuyenda mʼnjira iliyonse yoyipa kuti ndithe kumvera mawu anu. Onani mutuwo |