Masalimo 118:13 - Buku Lopatulika13 Kundikankha anandikankha ndikadagwa; koma Yehova anandithandiza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Kundikankha anandikankha ndikadagwa; koma Yehova anandithandiza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Adandikankha kwambiri, kotero kuti ndinali pafupi kugwa, koma Chauta adandithandiza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Anandikankha uku ndi uko ndipo ndinali pafupi kugwa, koma Yehova anandithandiza. Onani mutuwo |